3 Ine ndakwiyira kwambiri abusa,
Ndipo atsogoleri awo opondereza ndiwaimba mlandu.
Chifukwa ine Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndacheukira gulu langa la nkhosa+ lomwe ndi nyumba ya Yuda
Ndipo ndalisandutsa hatchi yanga yaulemerero, yokwera popita kunkhondo.