3 “Mkwiyo wanga wayakira abusa,+ ndipo atsogoleri awo oipa ngati mbuzi+ ndiwaimba mlandu.+ Pakuti ine Yehova wa makamu ndacheukira gulu langa la nkhosa.+ Ndacheukira nyumba ya Yuda ndipo ndaisandutsa hatchi+ yanga yaulemerero, yokwera popita kunkhondo.