Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 56:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo ndi agalu adyera kwambiri+ ndipo sakhuta,+ komanso ndi abusa osamvetsa zinthu.+ Aliyense wa iwo wapatukira kunjira yake n’cholinga chopeza phindu lachinyengo lochokera m’dera lake.+ Iwo amati:

  • Yeremiya 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Abusa achita zinthu mopanda nzeru,+ ndipo sanayese n’komwe kufunafuna Yehova.+ N’chifukwa chake sanachite zinthu mozindikira, ndipo ziweto zawo zonse zabalalika.”+

  • Ezekieli 34:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa chifukwa chimenechi ine ndilanga abusawo.+ Ndiwauza kuti andibwezere nkhosa zanga ndipo ndiwaletsa kudyetsa nkhosa zangazo.+ Abusawo sadzadzidyetsanso okha.+ Ndidzalanditsa nkhosa zanga kukamwa kwawo ndipo sizidzakhalanso chakudya chawo.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena