Ezekieli 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Pakuti amuna inu mwalankhula zabodza ndipo mwaona masomphenya onama, ine ndithana nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.” Zekariya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Mkwiyo wanga wayakira abusa,+ ndipo atsogoleri awo oipa ngati mbuzi+ ndiwaimba mlandu.+ Pakuti ine Yehova wa makamu ndacheukira gulu langa la nkhosa.+ Ndacheukira nyumba ya Yuda ndipo ndaisandutsa hatchi+ yanga yaulemerero, yokwera popita kunkhondo.
8 “‘Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “‘Pakuti amuna inu mwalankhula zabodza ndipo mwaona masomphenya onama, ine ndithana nanu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
3 “Mkwiyo wanga wayakira abusa,+ ndipo atsogoleri awo oipa ngati mbuzi+ ndiwaimba mlandu.+ Pakuti ine Yehova wa makamu ndacheukira gulu langa la nkhosa.+ Ndacheukira nyumba ya Yuda ndipo ndaisandutsa hatchi+ yanga yaulemerero, yokwera popita kunkhondo.