Ezekieli 23:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kuwonjezera apo, akaziwo atatumiza uthenga kwa amuna ochokera kutali, amuna amene anawatumizira uthengawo+ anabweradi.+ Iwe unasamba,+ n’kupaka zodzikongoletsera m’maso,+ ndi kuvala zodzikongoletsera kuti amuna amenewa akuone.+
40 Kuwonjezera apo, akaziwo atatumiza uthenga kwa amuna ochokera kutali, amuna amene anawatumizira uthengawo+ anabweradi.+ Iwe unasamba,+ n’kupaka zodzikongoletsera m’maso,+ ndi kuvala zodzikongoletsera kuti amuna amenewa akuone.+