2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+