2 Mafumu 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu,+ chifukwa anakwatira+ mwana wa Ahabu. Choncho iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+
18 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu,+ chifukwa anakwatira+ mwana wa Ahabu. Choncho iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.
14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+