13 koma wayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ n’kuchititsa Yuda ndi anthu okhala mu Yerusalemu kuchita zoipa,+ monga mmene a m’nyumba ya Ahabu anachititsira ena kuchita zoipa,+ ndiponso wapha ngakhale abale ako a m’nyumba ya bambo ako amene anali abwino kuposa iwe,+