2 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+ 2 Mbiri 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso iye anamanga malo okwezeka+ m’mapiri a ku Yuda kuti achititse anthu okhala mu Yerusalemu kuchita zoipa,+ ndiponso kuti asocheretse Yuda.+
22 Yehoramu atangoona Yehu, nthawi yomweyo anam’funsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji+ pali dama la Yezebeli+ mayi ako ndi amatsenga ake ambirimbiri?”+
11 Komanso iye anamanga malo okwezeka+ m’mapiri a ku Yuda kuti achititse anthu okhala mu Yerusalemu kuchita zoipa,+ ndiponso kuti asocheretse Yuda.+