Yesaya 48:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wanena kuti, “Oipa alibe mtendere.”+ Yesaya 57:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Oipa alibe mtendere,”+ akutero Mulungu wanga. Yesaya 59:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo amangonyalanyaza njira yamtendere,+ ndipo m’njira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.+ Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+ Yeremiya 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Yehova wanena kuti, ‘Usalowe m’nyumba imene olira maliro akuchitiramo phwando, ndipo usapite kukalira nawo maliro kapena kuwamvera chisoni.’+ “‘Pakuti anthu awa ndawachotsera mtendere wanga, kukoma mtima kosatha ndi chifundo,’+ watero Yehova. Aroma 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 ndipo sadziwa njira ya mtendere.”+
8 Iwo amangonyalanyaza njira yamtendere,+ ndipo m’njira zawo mulibe chilungamo.+ Misewu yawo aikhotetsakhotetsa.+ Palibe munthu aliyense woyenda mmenemo amene adzadziwe mtendere.+
5 “Yehova wanena kuti, ‘Usalowe m’nyumba imene olira maliro akuchitiramo phwando, ndipo usapite kukalira nawo maliro kapena kuwamvera chisoni.’+ “‘Pakuti anthu awa ndawachotsera mtendere wanga, kukoma mtima kosatha ndi chifundo,’+ watero Yehova.