Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 31:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo mkwiyo wanga udzawayakira tsiku limenelo,+ ndipo ndidzawasiya+ ndi kuwabisira nkhope yanga,+ motero adzakhala chinthu choyenera kuwonongedwa. Masoka ndi zowawa zambiri zidzawagwera,+ ndipo pa tsiku limenelo adzanena kuti, ‘Masoka amenewatu akutigwera chifukwa chakuti Mulungu wathu sali pakati pathu.’+

  • 2 Mbiri 15:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthuwo anagonjetsana chifukwa anaukirana okhaokha. Fuko limodzi linkamenyana ndi fuko lina+ ndiponso mzinda ndi mzinda wina, popeza Mulungu anawasiya pa chisokonezo ndi zowawa zosiyanasiyana.+

  • Yesaya 27:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tinthambi take tikadzauma, akazi obwera kumeneko adzatithyola n’kutiyatsa.+ Pakuti anthuwo si omvetsa zinthu.+ N’chifukwa chake yemwe anawapanga sadzawachitira chifundo, ndipo yemwe anawaumba sadzawakomera mtima.+

  • Yesaya 63:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma iwo anapanduka+ ndi kukhumudwitsa mzimu wake woyera.+ Chotero iye anasintha n’kukhala mdani+ wawo ndipo anachita nawo nkhondo.+

  • Zekariya 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Masiku amenewo asanafike, anthu ndi ziweto sanali kulandira malipiro.+ Munthu wa pa ulendo, adani anali kumusowetsa mtendere,+ chifukwa ine ndinali kuyambanitsa anthu onse.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena