Ezekieli 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Iwe mwana wa munthu, ine ndimenya+ chinthu chako chokongola ndi kuchichotsa kwa iwe.+ Koma iwe usadzigugude pachifuwa, kulira kapena kugwetsa misozi.+
16 “Iwe mwana wa munthu, ine ndimenya+ chinthu chako chokongola ndi kuchichotsa kwa iwe.+ Koma iwe usadzigugude pachifuwa, kulira kapena kugwetsa misozi.+