-
Ezekieli 24:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 M’mawa ndinayamba kulankhula ndi anthu ndipo pofika madzulo, mkazi wanga anamwalira. Ndiyeno m’mawa ndinachita zimene anandilamula.
-
-
Ezekieli 24:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 ‘Uza nyumba ya Isiraeli kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndidetsa malo anga opatulika,+ chinthu chimene mumachinyadira kwambiri,+ chinthu chosiririka kwa inu,+ ndiponso chinthu chimene mumachichitira chifundo. Ana anu aamuna ndi aakazi amene munawasiya m’mbuyo adzaphedwa ndi lupanga.+
-