Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “‘Munthu wotembenukira kwa olankhula ndi mizimu+ ndi olosera zam’tsogolo,+ komwe n’kuchita mosakhulupirika kwa ine,* ndidzam’kana ndithu ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+

  • Deuteronomo 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakati panu pasapezeke munthu wotentha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ wochita zamatsenga,+ woombeza,*+ wanyanga,+

  • 1 Mafumu 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tsopano tumizani uthenga ndipo musonkhanitse Aisiraeli onse kwa ine paphiri la Karimeli.+ Musonkhanitsenso aneneri 450 a Baala+ ndi aneneri 400 a mzati wopatulika,+ amene amadya patebulo la Yezebeli.”+

  • Malaki 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Anthu inu ndidzakuyandikirani kuti ndikuweruzeni.+ Sindidzazengereza kupereka umboni+ wotsutsa amatsenga,+ achigololo,+ olumbira monama+ komanso ochita chinyengo pa malipiro a munthu waganyu.+ Sindidzazengereza kupereka umboni wotsutsa anthu ochitira chinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye*+ ndiponso opondereza alendo.+ Anthu amenewa sakundiopa,”+ watero Yehova wa makamu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena