2 Mafumu 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ahaziya anayamba kulamulira ali ndi zaka 22 ndipo analamulira ku Yerusalemu chaka chimodzi.+ Mayi ake dzina lawo linali Ataliya+ mdzukulu wa Omuri+ mfumu ya Isiraeli. 2 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehosafati anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero waukulu,+ koma anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Ahabu.+ 2 Mbiri 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa anakwatira mwana wa Ahabu.+ Ndipo iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+
26 Ahaziya anayamba kulamulira ali ndi zaka 22 ndipo analamulira ku Yerusalemu chaka chimodzi.+ Mayi ake dzina lawo linali Ataliya+ mdzukulu wa Omuri+ mfumu ya Isiraeli.
18 Yehosafati anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero waukulu,+ koma anachita mgwirizano wa ukwati+ ndi Ahabu.+
6 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu, chifukwa anakwatira mwana wa Ahabu.+ Ndipo iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+