Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 16:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Patapita nthawi, anthu mumsasawo anamva kuti: “Zimiri wachitira chiwembu mfumu ndipo waipha.” Choncho tsiku limenelo, Aisiraeli onse omwe anali kumsasako anaveka ufumu Omuri,+ mkulu wa asilikali, kuti akhale mfumu ya Isiraeli.

  • 1 Mafumu 16:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 M’chaka cha 31 cha Asa mfumu ya Yuda, Omuri anakhala mfumu ya Isiraeli ndipo analamulira zaka 12. Ku Tiriza analamulirako zaka 6.

  • 1 Mafumu 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Nkhani zina zokhudza Omuri, zimene anachita ndi zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.

  • 2 Mbiri 22:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye anayamba kulamulira+ ali ndi zaka 22 ndipo analamulira ku Yerusalemu chaka chimodzi. Amayi ake dzina lawo linali Ataliya+ mdzukulu wa Omuri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena