2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Ataliya,+ mayi wa Ahaziya+ ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu.+ 2 Mafumu 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ataliya atamva anthu akuchita phokoso komanso akuthamanga, nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.+
13 Ataliya atamva anthu akuchita phokoso komanso akuthamanga, nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.+