2 Mafumu 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu,+ chifukwa anakwatira+ mwana wa Ahabu. Choncho iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova. 2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Ataliya,+ mayi wa Ahaziya+ ataona kuti mwana wake wafa, anapha ana onse achifumu.+ 2 Mafumu 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ataliya atamva anthu akuchita phokoso komanso akuthamanga, nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.+ 2 Mafumu 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anamugwira n’kumutulutsira pakhomo la kunyumba ya mfumu+ lolowera mahatchi,+ ndipo anam’phera pamenepo.+
18 Iye anayenda m’njira ya mafumu a Isiraeli+ monga mmene ankachitira a m’nyumba ya Ahabu,+ chifukwa anakwatira+ mwana wa Ahabu. Choncho iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.
13 Ataliya atamva anthu akuchita phokoso komanso akuthamanga, nthawi yomweyo anapita kwa anthu amene anali panyumba ya Yehova.+
16 Choncho anamugwira n’kumutulutsira pakhomo la kunyumba ya mfumu+ lolowera mahatchi,+ ndipo anam’phera pamenepo.+