2 Mafumu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo ankapereka ndalama zimene awerengazo kwa anthu ogwira ntchito+ amene anaikidwa panyumba ya Yehova. Anthu ogwira ntchitowo ankagwiritsa ntchito ndalamazo polipira amisiri a matabwa, omanga amene anali kugwira ntchito panyumba ya Yehovayo,
11 Iwo ankapereka ndalama zimene awerengazo kwa anthu ogwira ntchito+ amene anaikidwa panyumba ya Yehova. Anthu ogwira ntchitowo ankagwiritsa ntchito ndalamazo polipira amisiri a matabwa, omanga amene anali kugwira ntchito panyumba ya Yehovayo,