Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+ Salimo 102:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa cha kudzudzula kwanu kwamphamvu ndi mkwiyo wanu.+Inu mwandikweza m’mwamba kuti munditaye.+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
10 Chifukwa cha kudzudzula kwanu kwamphamvu ndi mkwiyo wanu.+Inu mwandikweza m’mwamba kuti munditaye.+