Salimo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, chifukwa chakuti munandikomera mtima munakhazikitsa mwamphamvu phiri langa.+Pamene munabisa nkhope yanu, ndinasokonezeka.+ Salimo 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Palibe pabwino m’thupi langa chifukwa cha chidzudzulo chanu.+Ndipo m’mafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+ Salimo 90:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti ife tatha chifukwa cha mkwiyo wanu,+Ndipo tasokonezeka chifukwa cha kupsa mtima kwanu.+
7 Inu Yehova, chifukwa chakuti munandikomera mtima munakhazikitsa mwamphamvu phiri langa.+Pamene munabisa nkhope yanu, ndinasokonezeka.+
3 Palibe pabwino m’thupi langa chifukwa cha chidzudzulo chanu.+Ndipo m’mafupa anga mulibe mtendere chifukwa cha tchimo langa.+