Yobu 34:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iye akachititsa bata, ndani angamudzudzule?Ndipo akabisa nkhope yake,+ ndani angamuone?Kaya abisire nkhope yake mtundu+ kapena munthu, n’chimodzimodzi. Salimo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+ Salimo 143:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+
29 Iye akachititsa bata, ndani angamudzudzule?Ndipo akabisa nkhope yake,+ ndani angamuone?Kaya abisire nkhope yake mtundu+ kapena munthu, n’chimodzimodzi.
10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+
7 Fulumirani, ndiyankheni inu Yehova.+Mphamvu zanga zatha.+Musandibisire nkhope yanu,+Chifukwa mukatero ndikhala ngati anthu amene akutsikira kudzenje la manda.+