Salimo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Musandibisire nkhope yanu.+Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+Inu mukhale mthandizi wanga.+Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+ Salimo 30:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, chifukwa chakuti munandikomera mtima munakhazikitsa mwamphamvu phiri langa.+Pamene munabisa nkhope yanu, ndinasokonezeka.+
9 Musandibisire nkhope yanu.+Musabweze mtumiki wanu mutakwiya.+Inu mukhale mthandizi wanga.+Musanditaye ndi kundisiya, inu Mulungu wa chipulumutso changa.+
7 Inu Yehova, chifukwa chakuti munandikomera mtima munakhazikitsa mwamphamvu phiri langa.+Pamene munabisa nkhope yanu, ndinasokonezeka.+