Luka 11:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Kuyambira magazi a Abele+ mpaka magazi a Zekariya,+ amene anaphedwa pakati pa guwa lansembe ndi nyumba yopatulika.’+ Inde, ndikukuuzani, m’badwo uwu udzafunsidwa za magazi amenewo.
51 Kuyambira magazi a Abele+ mpaka magazi a Zekariya,+ amene anaphedwa pakati pa guwa lansembe ndi nyumba yopatulika.’+ Inde, ndikukuuzani, m’badwo uwu udzafunsidwa za magazi amenewo.