Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+
8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+