Yobu 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aliyense wosasonyeza mnzake kukoma mtima kosatha,+Adzasiyanso kuopa Wamphamvuyonse.+ Miyambo 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Aliyense wobwezera zoipa pa zabwino,+ zoipa sizidzachoka panyumba pake.+