1 Mafumu 7:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anaika zotengera zisanu mbali ya kudzanja lamanja kwa nyumbayo ndi zotengera zina zisanu mbali ya kumanzere kwa nyumbayo.+ Thanki ija anaiika mbali ya kudzanja lamanja kwa nyumbayo, kum’mawa chakum’mwera kwake.+
39 Anaika zotengera zisanu mbali ya kudzanja lamanja kwa nyumbayo ndi zotengera zina zisanu mbali ya kumanzere kwa nyumbayo.+ Thanki ija anaiika mbali ya kudzanja lamanja kwa nyumbayo, kum’mawa chakum’mwera kwake.+