Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Uike Aroni ndi ana ake kukhala ansembe, kuti azigwira ntchito yaunsembe.+ Aliyense amene si Mlevi akayandikira malowo, aziphedwa.”+

  • Numeri 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iweyo ndi ana ako, muzichita utumiki wanu waunsembe mosamala pa chilichonse chokhudza guwa lansembe, ndiponso pa zonse zamkati, kuseri kwa nsalu yotchinga.+ Umenewu ndiwo utumiki wanu.+ Unsembewu ndikukupatsani monga mphatso, ndipo aliyense wosakhala Mlevi akayandikira pafupi aziphedwa.”+

  • 1 Samueli 2:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 “‘N’chifukwa chake Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ndinanenadi kuti, A m’nyumba yako ndiponso a m’nyumba ya kholo lako adzanditumikira mpaka kalekale.”+ Koma tsopano Yehova akuti: “Sindingachitenso zimenezo, chifukwa amene akundilemekeza+ ndiwalemekeza,+ koma amene akundinyoza ndi opanda pake kwa ine.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena