Ekisodo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+ 1 Mafumu 7:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa, ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.
3 Kenako upange ndowa zake zochotsera phulusa losakanizika ndi mafuta, mafosholo ake, mbale zake zolowa, mafoloko aakulu, ndi zopalira moto zake. Ziwiya zake zonse uzipange ndi mkuwa.+
45 ndowa, mafosholo, mbale zolowa, ndi ziwiya zina zonse.+ Hiramu anapanga zinthu zimenezi ndi mkuwa wonyezimira. Anapangira Mfumu Solomo kuti aziike m’nyumba ya Yehova.