Levitiko 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, pamenepo ndidzakulangani mowirikiza ka 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.+ Deuteronomo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+ 1 Samueli 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+Wotsitsa ndiponso Wokweza,+ Yobu 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uone wodzikweza aliyense n’kumuchepetsa,+Ndipo oipa uwaponderezere pamalo pomwe alilipo.
18 “‘Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, pamenepo ndidzakulangani mowirikiza ka 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.+
43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+
7 Yehova ndi Wopereka Umphawi+ ndi Wolemeretsa,+Wotsitsa ndiponso Wokweza,+ Yobu 40:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Uone wodzikweza aliyense n’kumuchepetsa,+Ndipo oipa uwaponderezere pamalo pomwe alilipo.