Ekisodo 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mose anaona kuti anthuwo akuchita zinthu motayirira, chifukwa Aroni anawalola kuchita zotayirira+ zomwe zinachititsa adani awo kuwatonza.+
25 Mose anaona kuti anthuwo akuchita zinthu motayirira, chifukwa Aroni anawalola kuchita zotayirira+ zomwe zinachititsa adani awo kuwatonza.+