2 Mbiri 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinatero chifukwa chakuti Yehova anatsitsa+ Yuda chifukwa cha Ahazi mfumu ya Isiraeli, popeza analekerera kuti makhalidwe oipa achuluke mu Yuda.+ Iye anachita zinthu zambiri zosakhulupirika kwa Yehova.
19 Zinatero chifukwa chakuti Yehova anatsitsa+ Yuda chifukwa cha Ahazi mfumu ya Isiraeli, popeza analekerera kuti makhalidwe oipa achuluke mu Yuda.+ Iye anachita zinthu zambiri zosakhulupirika kwa Yehova.