2 Mafumu 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mfumuyo itabwerako ku Damasiko, inaliona guwa lansembelo, ndipo inayamba kupita kuguwalo+ kukapereka nsembe.+ 2 Mafumu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Paguwa lansembelo, mfumuyo inapitiriza kuwotchapo+ nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu,+ ndi kuthirapo nsembe yachakumwa+ ndiponso kuwazapo magazi a nsembe zake zachiyanjano.
12 Mfumuyo itabwerako ku Damasiko, inaliona guwa lansembelo, ndipo inayamba kupita kuguwalo+ kukapereka nsembe.+
13 Paguwa lansembelo, mfumuyo inapitiriza kuwotchapo+ nsembe yopsereza+ ndi nsembe yambewu,+ ndi kuthirapo nsembe yachakumwa+ ndiponso kuwazapo magazi a nsembe zake zachiyanjano.