Numeri 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Muwerenge ana onse a Kohati+ mwa ana a Levi, malinga ndi mabanja a nyumba za makolo awo. 1 Mbiri 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa ana a Kohati panali Uriyeli+ mtsogoleri wawo ndi abale ake okwanira 120. 1 Mbiri 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Kohati+ analipo anayi. Panali Amuramu, Izara,+ Heburoni+ ndi Uziyeli.+