Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+

  • Levitiko 4:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ndipo tchimo limene achitalo ladziwika,+ pamenepo mpingowo uzipereka ng’ombe yaing’ono yamphongo monga nsembe yamachimo, azibwera nayo pakhomo la chihema chokumanako.

  • Numeri 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Koma ngati mwachita cholakwa cholephera kusunga malamulo onsewa+ amene Yehova walankhula kudzera mwa Mose,

  • Numeri 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ngati khamulo lachita cholakwacho mosazindikira, pamenepo khamu lonselo lipereke ng’ombe yaing’ono yamphongo monga nsembe yopsereza yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova. Apereke nsembeyo limodzi ndi nsembe yake yambewu ndiponso nsembe yake yachakumwa monga mwa dongosolo la nthawi zonse.+ Aperekenso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena