-
Ezara 8:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Anthu amene anabwera kuchokera ku ukapolo,+ amene kale anali m’dziko la eni, anapereka nsembe zopsereza+ kwa Mulungu wa Isiraeli. Anapereka ng’ombe zamphongo 12+ za Aisiraeli onse, nkhosa zamphongo 96,+ ana a nkhosa amphongo 77, ndi mbuzi zamphongo 12+ monga nsembe yamachimo. Zonsezi anazipereka monga nsembe yopsereza kwa Yehova.
-