Numeri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsopano Yehova analankhula ndi Aroni kuti: “Iwe ndi ana ako, ndi nyumba yonse ya bambo ako, mudzasenza zolakwa zanu pa malamulo okhudza malo opatulika.+ Iweyo ndi ana ako mudzasenza zolakwa zanu pa malamulo okhudza unsembe wanu.+
18 Tsopano Yehova analankhula ndi Aroni kuti: “Iwe ndi ana ako, ndi nyumba yonse ya bambo ako, mudzasenza zolakwa zanu pa malamulo okhudza malo opatulika.+ Iweyo ndi ana ako mudzasenza zolakwa zanu pa malamulo okhudza unsembe wanu.+