Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+ Levitiko 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Asatuluke m’malo opatulika ndipo asadetse malo opatulika a Mulungu wake,+ chifukwa pamutu pake pali chizindikiro cha kudzipereka ndi mafuta odzozera a Mulungu wake.+ Ine ndine Yehova.
12 Asatuluke m’malo opatulika ndipo asadetse malo opatulika a Mulungu wake,+ chifukwa pamutu pake pali chizindikiro cha kudzipereka ndi mafuta odzozera a Mulungu wake.+ Ine ndine Yehova.