7 Musachoke pakhomo la chihema chokumanako kuopera kuti mungafe,+ chifukwa mwadzozedwa ndi mafuta odzozera a Yehova.”+ Choncho iwo anachita monga mwa mawu a Mose.
23 Koma asayandikire nsalu yotchinga+ ndiponso guwa lansembe,+ chifukwa iye ali ndi chilema.+ Asaipitse malo anga opatulika,+ chifukwa ine ndine Yehova amene ndikuwapatula kuti akhale oyera.’”+