Levitiko 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Lankhula ndi Aroni kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana ako, ku mibadwo yawo yonse, amene ali ndi chilema+ asayandikire malo opatulika kudzapereka mkate wa Mulungu wake.+
17 “Lankhula ndi Aroni kuti, ‘Munthu aliyense mwa ana ako, ku mibadwo yawo yonse, amene ali ndi chilema+ asayandikire malo opatulika kudzapereka mkate wa Mulungu wake.+