12Chotero ndikukudandaulirani mwa chifundo chachikulu cha Mulungu abale, kuti mupereke matupi anu+ ngati nsembe+ yamoyo,+ yoyera+ ndi yovomerezeka kwa Mulungu,+ ndiyo utumiki wopatulika+ mwa kugwiritsa ntchito luntha la kuganiza.+
26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+