Aefeso 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 imene waigwiritsa ntchito pa Khristu pamene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumukhazika kudzanja lake lamanja+ m’malo akumwamba.+ Aheberi 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero, popeza tili ndi mkulu wa ansembe wapamwamba, Yesu Mwana wa Mulungu,+ amene anapita kumwamba,+ tiyeni tipitirize kulengeza chikhulupiriro chathu mwa iye.+ 1 Petulo 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ pakuti anapita kumwamba, ndipo angelo,+ maulamuliro, ndi mphamvu zinakhala pansi pake.+
20 imene waigwiritsa ntchito pa Khristu pamene anamuukitsa kwa akufa+ ndi kumukhazika kudzanja lake lamanja+ m’malo akumwamba.+
14 Chotero, popeza tili ndi mkulu wa ansembe wapamwamba, Yesu Mwana wa Mulungu,+ amene anapita kumwamba,+ tiyeni tipitirize kulengeza chikhulupiriro chathu mwa iye.+
22 Iye ali kudzanja lamanja la Mulungu,+ pakuti anapita kumwamba, ndipo angelo,+ maulamuliro, ndi mphamvu zinakhala pansi pake.+