Aefeso 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ndipo anatikweza+ pamodzi, ndi kutikhazika pamodzi m’malo akumwamba+ mogwirizana ndi Khristu Yesu. Aheberi 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+
26 Pakuti mkulu wa ansembe ngati ameneyu ndiyedi wotiyenerera.+ Iye ndi wokhulupirika,+ wosalakwa,+ wosaipitsidwa,+ wosiyana ndi anthu ochimwa,+ ndipo wakwera pamwamba kwambiri kuposa kumwamba.+