Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+ Aheberi 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tiyeni tipitirize kulengeza poyera chiyembekezo+ chathu ndipo tisagwedezeke,+ pakuti amene anapereka lonjezo lija ndi wokhulupirika.+
3 Chotero, abale athu oyera, amene muli nawo m’gulu la oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi+ ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
23 Tiyeni tipitirize kulengeza poyera chiyembekezo+ chathu ndipo tisagwedezeke,+ pakuti amene anapereka lonjezo lija ndi wokhulupirika.+