Aheberi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Khristu monga Mwana+ wa mwiniwake wa nyumbayo, anali kuyang’anira nyumba ya Mulungu mokhulupirika. Ife ndife nyumba ya Mulunguyo,+ ngati tagwira mwamphamvu ufulu wathu wa kulankhula ndi kupitirizabe kunyadira chiyembekezocho mpaka mapeto.+ Aheberi 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chiyembekezo+ chimene tili nachochi chili ngati nangula* wa miyoyo yathu ndipo n’chotsimikizika ndiponso chokhazikika. Chiyembekezo chimenechi chimatilowetsa mkati, kuseri kwa nsalu yotchinga,+
6 Koma Khristu monga Mwana+ wa mwiniwake wa nyumbayo, anali kuyang’anira nyumba ya Mulungu mokhulupirika. Ife ndife nyumba ya Mulunguyo,+ ngati tagwira mwamphamvu ufulu wathu wa kulankhula ndi kupitirizabe kunyadira chiyembekezocho mpaka mapeto.+
19 Chiyembekezo+ chimene tili nachochi chili ngati nangula* wa miyoyo yathu ndipo n’chotsimikizika ndiponso chokhazikika. Chiyembekezo chimenechi chimatilowetsa mkati, kuseri kwa nsalu yotchinga,+