Mateyu 26:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Koma Yesu anangokhala chete.+ Chotero mkulu wa ansembe anati: “Ndikukulumbiritsa pali Mulungu wamoyo,+ utiuze ngati ndiwedi Khristu+ Mwana wa Mulungu!” Maliko 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+ Aheberi 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.
63 Koma Yesu anangokhala chete.+ Chotero mkulu wa ansembe anati: “Ndikukulumbiritsa pali Mulungu wamoyo,+ utiuze ngati ndiwedi Khristu+ Mwana wa Mulungu!”
11 Pamenepo panamveka mawu ochokera kumwamba akuti: “Iwe ndiwe Mwana wanga wokondedwa, ndimakondwera nawe.”+
2 Kumapeto kwa masiku ano,+ iye walankhulanso kwa ife kudzera mwa Mwana wake,+ amene anamuika kuti akhale wolandira zinthu zonse monga cholowa.+ Kudzera mwa iyeyu, Mulungu analenga+ nthawi* zosiyanasiyana.