Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi+ monga nsembe yamachimo, ndi ana a nkhosa amphongo awiri, aliyense wachaka chimodzi, monga nsembe yachiyanjano.+

  • Numeri 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ngati khamulo lachita cholakwacho mosazindikira, pamenepo khamu lonselo lipereke ng’ombe yaing’ono yamphongo monga nsembe yopsereza yafungo lokhazika mtima pansi kwa Yehova. Apereke nsembeyo limodzi ndi nsembe yake yambewu ndiponso nsembe yake yachakumwa monga mwa dongosolo la nthawi zonse.+ Aperekenso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo.+

  • Numeri 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Muziperekanso mwana wa mbuzi+ monga nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.+

  • Numeri 29:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi wamphongo, monga nsembe yamachimo yophimbira machimo anu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena