Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. 2 Mbiri 29:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nsembe zopsereza zimene mpingowo unabweretsa zinakwana ng’ombe 70, nkhosa zamphongo 100, ndi ana a nkhosa amphongo 200. Zonsezi anazipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza.+
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
32 Nsembe zopsereza zimene mpingowo unabweretsa zinakwana ng’ombe 70, nkhosa zamphongo 100, ndi ana a nkhosa amphongo 200. Zonsezi anazipereka kwa Yehova monga nsembe yopsereza.+