2 Mbiri 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pambuyo pake, anthu onse anapita kukachisi wa Baala n’kukamugwetsa+ ndipo anagwetsanso maguwa ake ansembe.+ Mafano ake anawaphwanyaphwanya,+ ndipo Mateni+ wansembe wa Baala anamupha+ patsogolo pa maguwa ansembewo.
17 Pambuyo pake, anthu onse anapita kukachisi wa Baala n’kukamugwetsa+ ndipo anagwetsanso maguwa ake ansembe.+ Mafano ake anawaphwanyaphwanya,+ ndipo Mateni+ wansembe wa Baala anamupha+ patsogolo pa maguwa ansembewo.