2 Mbiri 30:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Hezekiya mfumu ya Yuda anapereka+ ku mpingowo ng’ombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 7,000. Akalonganso+ anapereka ku mpingowo ng’ombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 10,000, ndipo ansembe+ ambiri anali kudziyeretsa.
24 Hezekiya mfumu ya Yuda anapereka+ ku mpingowo ng’ombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 7,000. Akalonganso+ anapereka ku mpingowo ng’ombe zamphongo 1,000 ndi nkhosa 10,000, ndipo ansembe+ ambiri anali kudziyeretsa.